" Freely you have received, freely give " (Matthew 10:8)

НАЧАЛНА СТРАНИЦА   |  КАРТА НА САЙТА  |  КОНТАКТИ C HAC  |  ПОМОЩ    
Проучване на Библията Безплатни християнски книги Безплатни християнски е-книги За нас
  БЕЗПЛАТНА e-книжна версия на чичева език издание 22

 

Chifuniro Cha Utatu Oyera Ku Anthu
- Ziphunzitso pa Genesis (I)

 • Електронната книга на формата : Acrobat PDF Reader
 • Текущи Изтегляния : 0
 • За тази книга
 • Съдържание
 

Kulengeza:

Chifuniro cha Utatu Oyera ku Anthu

Kufothokoza:

Mu Buku la Genesis, cholinga cimene Mulungu anatilengera chikupezeka. Ngati omanga manyumba apanga maonekedwe a nyumba kapena olemba ailemba, poyamba akukhala ndi nchito imene adzakwanilitsidwa mu maganizo awo sanayambedi kugwira nchito pa nchito yawoyo. Momwemo, Mulungu wathu nayenso anali nacho chipulumutso chathu mu maganizo Ache cha anthu ngakhalenso asanalenge kumwamba ndi dziko lapansi, ndipo Iye anapanga Adamu ndi Eve mwa cholingachi mu maganizo. Mulungu anali kufuna kumasulira kwa ife a malo a Kumwamba, amene sakuoneka ndi maso athu a thupi, mwakupanga chifanizo cha malo a padziko lapansi cimene tonse tingachione ndi kuchimvetsetsa.
Ngakhalenso dziko lisanakhalepo, Mulungu anali kufuna kupulumutsa anthu mwa ngwiro mwa kuwapatsa uthenga wa madzi ndi Mzimu ku mtima wa munthu aliyense. Chotero ngakhale kuti anthu onse anapangidwa kuchoka kufumbi, ayenera kuphunzira ndi kudziwa Choonadi cha uthenga wa madzi ndi Mzimu kuti aphindulire miyoyo yawo. Ngati anthu akupitiliza kukhala kopanda kudziwa ulamuliro wa Kumwamba, adzataya osati zinthu zokha zadziko lapansi, komanso zinthu zonse zimene zili Kumwamba.

Mau a wosindikiza:

Paulo akumasulira za choonadi cha Yesu mnjira yosabvuta ndipo anthu ambiri akukonda m'mene akubwerapo pa zinthu mobwerezabwereza. Kupitira mu bukuli achipanga kukhala chosabvuta ku oyera kuti aphunzitse ena m'mene angabadwire mwatsopano. N’buku lalikuli ku oyera kuti aphunzitse nalo ndipo ndi buku lalikulu ku aja amene akufuna kubadwa mwatsopano. Tikuthokoza Mulungu pam’pata wabwinowu umene tapatsidwa kuti tiwerenge mabukuwa.


 

 
Безплатни християнски е-книги
    Списък на е-книгите
    чичева издание 22
 
 • За тази книга
 •  
 • Съдържание
 •     Какво e е-книга?
   
 • За е-книгата
 •  
 • Как да чета е-книга?
 •  
 • Често задавани въпроси
 •  
 • Помощ за изтегляне
 •     Четци за е-книги
   
 • MS Reader 2.0
 •  
 • Acrobat Reader 4.0
 •  

  Регистрирай се като сътрудник
  Зоната на съдружника
  Bookmark
     
  Copyright © 2001 - 2019 The New Life Mission. All Rights Reserved.